Phone Kwa Mkazi Wakale

Samuel Sawelengera
Released: 30 September, 2020   ·   1212°C Warm   ·   0   ·   2

Description

Ndakatulo yomwe ikuphuzitsa kuti amuna tisamakhale odudukira zili zonse ponyoza mkazi wako pa mbuyo umazamufuna ndipo amakhala kuti nayenso wakuyiwala ali ndi wina.
3
guest
0 Comments
Inline Feedbacks
View all comments


Artist: Samuel Sawelengera

Poems published: 15

View all poems