Ndathawako Kwa Satana

Novemba
Released: 8 June, 2020   ·   566°C Cool   ·   0   ·   0

Description

Ndakatulo yofotokoza za munthu yemwe akhala akuchita zinthu zoipa kapena zosayenera pamaso pa Mulungu koma pozindikira za zomwe Chauta amuonetsera kapena zomwe iye mwini wake waziona anapanga chisankho chosiya zonse zija ndikuyamba kutsata ambuye.
3
guest
0 Comments
Inline Feedbacks
View all comments