Henderson Mmangeni – Kutaliko

Mlakatuli Wamanyazi Henderson Mmangeni
Released: 24 November, 2017   ·   2358°C Hot   ·   0   ·   0

Description

Ndakatulo yofotokoza za mfuwu womveka patali kuchokera kwa amayi komanso asungwana ochitidwa nkhaza. Ndakatuloyi ikumaliza nkufuula kuti tileke nkhaza kwa amayi ndi asungwana chifukwa nzachabe.
2
guest
0 Comments
Inline Feedbacks
View all comments


Artist: Mlakatuli Wamanyazi Henderson Mmangeni

Poems published: 8

View all poems