Tonkhwetonkhwe
Desmond Galafa
Description
Tonkhwetonkhwe ndi imodzi mwa ndakatulo zosiyanasiyana zomwe mlakatuli Desmond Galafa akusonkhanitsa. Cholinga chake ndichakuti zonsezi zikathere kotulutsa chimbale chothyakuka bwino momwenso mukhale ndakatulo zokhudza nkhani zosiyanasiyana.