Released: 27 May, 2016 ·
69365°C
Extremely hot
·
28
·
159
Description
A passionate and patriotic Malawi National Football Team fan's cry on the Team's underachievements and a call for reforms on the same for better results and performances.
Team yochitsa manyazi ngati iyi nsinayiwonepo,ndipo sukunama flames sidzamva..nkhutukumve zamaplayer
chikondi
6 years ago
nice 1
Joseph Chikabadwa
6 years ago
Ooh Ooh tso dala apa nde mwalasatu mwangugundilatu nthiti za mbawala ya belemuda wa chisoti cha chidendene cha paka, vumbwe wa sokosi ya bondo la boot la gaba wa chitete cha ludzu la mphopo ya chigoli chothetsa chipemba cha akapuku osuzumira mumphika wa bwato la masewera a mphira wa mapaz monga braz amanenera anyamata awa wawo ukhale mpira wamapazi basi kkkkkk zamiyendo lekelani ana a Comrade ujayu mdala okakamila ntchito kuchembera take tiwana tinakakamila a Mutharika wana onyentchera kamba ka njala ati yodza kamba ka eleninyo mkuti nchiyani Eleninyoyo mpaka Mtawali ma plan kutha phwi ? angulekani dala muzikalisha ng’ombe… Read more »
Lifeyo Chitukula
6 years ago
Zoonadi flames sidzanva mbuli zokhazokha
Afana muli boo ife kuno Ku China Guangzhou province tili pambuyo panu man Robs
This is real art.. Brilliant 👌
thank God for the talent.awa sazamvadi
Chiwamba amatha. Currently he’s the best,KING of poetry in Malawi
Flames inali kale ndithu. pano or Djibouti itha kutisambitsa nazo zigoli
This is great bro, nice poem!!! Calling a spade a spade. Keep it up!! Umandisangalatsa munthu wamkulu with your great poems.
Nice one…. Flames need to change
Classic
100% correct Kusapota flames nkubesa!
This is nice Chiwamba, Flames dissapoints
Zili khenge man Chiwamba…umatha!
Anyamata ayesetsa dzulo zangovuta
kkkkkkkkkk
Team yochitsa manyazi ngati iyi nsinayiwonepo,ndipo sukunama flames sidzamva..nkhutukumve zamaplayer
nice 1
Ooh Ooh tso dala apa nde mwalasatu mwangugundilatu nthiti za mbawala ya belemuda wa chisoti cha chidendene cha paka, vumbwe wa sokosi ya bondo la boot la gaba wa chitete cha ludzu la mphopo ya chigoli chothetsa chipemba cha akapuku osuzumira mumphika wa bwato la masewera a mphira wa mapaz monga braz amanenera anyamata awa wawo ukhale mpira wamapazi basi kkkkkk zamiyendo lekelani ana a Comrade ujayu mdala okakamila ntchito kuchembera take tiwana tinakakamila a Mutharika wana onyentchera kamba ka njala ati yodza kamba ka eleninyo mkuti nchiyani Eleninyoyo mpaka Mtawali ma plan kutha phwi ? angulekani dala muzikalisha ng’ombe… Read more »
Zoonadi flames sidzanva mbuli zokhazokha
Afana muli boo ife kuno Ku China Guangzhou province tili pambuyo panu man Robs
Munthu wamkulu zedi
Basi mawu njamweyo, Flames sidzamva.
I like it, kp it u deserve a credit
Kukhala m’malawi mkulimba mtima
Team tinabetsa iyi man. Big up Chiwamba!
Kawawa team in Gotha bas
Good stuff
Awa ndi makina mdala
I love the bluntness, I love the creativity, keep it up bro
You’re creative
Flames siimva
Wow, this packs a lot of heat – its literally on flames. The onomatopoeia, comedy and voice acting creates a perfect synergy