Flames Sidzamva

Robert Chiwamba Robert Chiwamba
Released: 27 May, 2016   ·   52663°C Extremely hot   ·   21   ·   129

Description

A passionate and patriotic Malawi National Football Team fan's cry on the Team's underachievements and a call for reforms on the same for better results and performances.

Drop a comment

21 Comments on "Flames Sidzamva"

avatar
Sort by:   newest | oldest | most voted
Khadija
Guest

This is real art.. Brilliant 👌

n athan
Guest

thank God for the talent.awa sazamvadi

Kai
Guest

Chiwamba amatha. Currently he’s the best,KING of poetry in Malawi

Sosten Mpinganjira
Guest

Flames inali kale ndithu. pano or Djibouti itha kutisambitsa nazo zigoli

Dominic Kapatamoyo
Guest

This is great bro, nice poem!!! Calling a spade a spade. Keep it up!! Umandisangalatsa munthu wamkulu with your great poems.

Yaya
Guest

Nice one…. Flames need to change

Misheck
Guest

Classic

Mattheuz
Guest

100% correct Kusapota flames nkubesa!

Kennedy Yakobe
Guest

This is nice Chiwamba, Flames dissapoints

osward mulenga
Guest

Zili khenge man Chiwamba…umatha!

Ernest Sapala
Guest

Anyamata ayesetsa dzulo zangovuta

Bernadetta pereya garrett
Guest
Bernadetta pereya garrett

Team yochitsa manyazi ngati iyi nsinayiwonepo,ndipo sukunama flames sidzamva..nkhutukumve zamaplayer

chikondi
Guest

nice 1

Joseph Chikabadwa
Guest
Ooh Ooh tso dala apa nde mwalasatu mwangugundilatu nthiti za mbawala ya belemuda wa chisoti cha chidendene cha paka, vumbwe wa sokosi ya bondo la boot la gaba wa chitete cha ludzu la mphopo ya chigoli chothetsa chipemba cha akapuku osuzumira mumphika wa bwato la masewera a mphira wa mapaz monga braz amanenera anyamata awa wawo ukhale mpira wamapazi basi kkkkkk zamiyendo lekelani ana a Comrade ujayu mdala okakamila ntchito kuchembera take tiwana tinakakamila a Mutharika wana onyentchera kamba ka njala ati yodza kamba ka eleninyo mkuti nchiyani Eleninyoyo mpaka Mtawali ma plan kutha phwi ? angulekani dala muzikalisha ng’ombe… Read more »
Lifeyo Chitukula
Guest

Zoonadi flames sidzanva mbuli zokhazokha
Afana muli boo ife kuno Ku China Guangzhou province tili pambuyo panu man Robs

Willard Mbewe
Guest

Munthu wamkulu zedi

metallic
Guest

I like it, kp it u deserve a credit

Kwenje
Guest

Kukhala m’malawi mkulimba mtima

Abono MA
Guest

Team tinabetsa iyi man. Big up Chiwamba!

wpDiscuz
Robert Chiwamba

Artist: Robert Chiwamba

Poems published: 18

View all poems